Numeri 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo, Yoswa mwana wa Nuni, yemwe anali mtumiki+ wa Mose kuyambira ali mnyamata, anayankhira kuti: “Mbuyanga Mose, kawaletseni amenewo!”+ Numeri 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni,+ ndi Kalebe mwana wa Yefune,+ amene anakazonda nawo dzikolo, anang’amba zovala zawo.+ Numeri 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Kalebe+ mwana wa Yefune Mkenizi, ndi Yoswa+ mwana wa Nuni, adzaiona nthakayo chifukwa akhala akumvera Yehova ndi mtima wonse.’ Deuteronomo 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yoswa mwana wa Nuni anali wodzazidwa ndi mzimu wa nzeru,+ pakuti Mose anaika manja ake pa iye.+ Choncho ana a Isiraeli anayamba kumumvera ndipo iwo anayamba kuchita monga momwe Yehova analamulira Mose.+
28 Pamenepo, Yoswa mwana wa Nuni, yemwe anali mtumiki+ wa Mose kuyambira ali mnyamata, anayankhira kuti: “Mbuyanga Mose, kawaletseni amenewo!”+
6 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni,+ ndi Kalebe mwana wa Yefune,+ amene anakazonda nawo dzikolo, anang’amba zovala zawo.+
12 Koma Kalebe+ mwana wa Yefune Mkenizi, ndi Yoswa+ mwana wa Nuni, adzaiona nthakayo chifukwa akhala akumvera Yehova ndi mtima wonse.’
9 Yoswa mwana wa Nuni anali wodzazidwa ndi mzimu wa nzeru,+ pakuti Mose anaika manja ake pa iye.+ Choncho ana a Isiraeli anayamba kumumvera ndipo iwo anayamba kuchita monga momwe Yehova analamulira Mose.+