Genesis 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako, malowo anawatcha Beteli.+ Koma dzina lakale la mzindawo linali Luzi.+ Yoswa 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atachoka ku Beteli wa ku Luzi,+ malirewo anakadutsa kumalire a Aareki+ ku Ataroti.