Numeri 1:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Onse olembedwa mayina a fuko la Aseri analipo 41,500.+ Numeri 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Asilikali ake olembedwa mayina alipo 41,500.+ Numeri 26:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Amenewa ndiwo anali mabanja a ana aamuna a Aseri.+ Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 53,400.+
47 Amenewa ndiwo anali mabanja a ana aamuna a Aseri.+ Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 53,400.+