Yoswa 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Aisiraeliwo ananyamuka n’kukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibeoni,+ Kefira,+ Beeroti,+ ndi Kiriyati-yearimu.+ Yoswa 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kuchokera m’fuko la Benjamini, anawapatsa Gibeoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Geba+ ndi malo ake odyetserako ziweto, 1 Mbiri 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma pa nthawiyo, chihema chopatulika cha Yehova chimene Mose anapanga m’chipululu ndi guwa lansembe zopsereza, zinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni.+
17 Pamenepo Aisiraeliwo ananyamuka n’kukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibeoni,+ Kefira,+ Beeroti,+ ndi Kiriyati-yearimu.+
17 Kuchokera m’fuko la Benjamini, anawapatsa Gibeoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Geba+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
29 Koma pa nthawiyo, chihema chopatulika cha Yehova chimene Mose anapanga m’chipululu ndi guwa lansembe zopsereza, zinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni.+