1 Mbiri 9:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Moza anabereka Bineya, Bineya anabereka Refaya,+ Refaya anabereka Eleasa, ndipo Eleasa anabereka Azeli.
43 Moza anabereka Bineya, Bineya anabereka Refaya,+ Refaya anabereka Eleasa, ndipo Eleasa anabereka Azeli.