Salimo 127:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndicho mphoto.+ Salimo 128:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mkazi wako adzakhala ngati mtengo wa mpesa wobala zipatso+Mkati mwa nyumba yako.Ana ako adzakhala ngati mphukira za mitengo ya maolivi+ kuzungulira tebulo lako. Salimo 128:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo uone ana a ana ako.+Mtendere ukhale pa Isiraeli.+
3 Mkazi wako adzakhala ngati mtengo wa mpesa wobala zipatso+Mkati mwa nyumba yako.Ana ako adzakhala ngati mphukira za mitengo ya maolivi+ kuzungulira tebulo lako.