1 Mbiri 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamara+ mpongozi wake ndiye anam’berekera Perezi+ ndi Zera. Ana onse a Yuda anali asanu. 1 Mbiri 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ana a Zera+ anali Zimiri, Etani, Hemani, Kalikoli, ndi Dara.+ Onse pamodzi analipo asanu.