9 Davide anayamba kukhala m’malo okhala mumpanda wolimba kwambiri, ndipo anawatcha Mzinda wa Davide. Iye anayamba kumanga malo onsewo kuyambira ku Chimulu cha Dothi*+ mpaka mkati.
10 Pamenepo Davide sanafunenso kutenga likasa la Yehova kupita nalo kumene iye anali kukhala, ku Mzinda wa Davide.+ Chotero Davide analipatutsira kunyumba ya Obedi-edomu+ Mgiti.+