1 Mbiri 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pinihasi+ mwana wa Eleazara+ ndiye anali mtsogoleri wawo kalekale, ndipo Yehova anali naye.+ Salimo 46:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.] Yesaya 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Konzani zochita, koma zidzalephereka.+ Nenani zoti anthu achite, koma sizidzachitidwa, chifukwa Mulungu ali nafe.+
7 Yehova wa makamu ali ndi ife.+Mulungu wa Yakobo ndiye malo athu okwezeka ndiponso achitetezo.+ [Seʹlah.]
10 Konzani zochita, koma zidzalephereka.+ Nenani zoti anthu achite, koma sizidzachitidwa, chifukwa Mulungu ali nafe.+