2 Samueli 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Patapita nthawi, Davide anafotokoza zimene anali kulakalaka kuti: “Ndikanakonda ndikanamwa madzi a m’chitsime cha ku Betelehemu chimene chili pachipata!”+
15 Patapita nthawi, Davide anafotokoza zimene anali kulakalaka kuti: “Ndikanakonda ndikanamwa madzi a m’chitsime cha ku Betelehemu chimene chili pachipata!”+