-
Nehemiya 9:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Munamuona kuti anali ndi mtima wokhulupirika pamaso panu.+ Chotero munachita naye pangano+ kuti mudzam’patsa dziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Aperezi, Ayebusi ndi Agirigasi. Munachita naye pangano kuti mudzapereka dziko limeneli kwa mbewu yake,+ ndipo munachitadi zimene munanena chifukwa ndinu wolungama.+
-