1 Samueli 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, kuchokera pamene Likasa linayamba kukhala ku Kiriyati-yearimu, panapita nthawi yaitali mpaka zinakwana zaka 20. Izi zili choncho, nyumba yonse ya Isiraeli inayamba kulirira Yehova.+
2 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, kuchokera pamene Likasa linayamba kukhala ku Kiriyati-yearimu, panapita nthawi yaitali mpaka zinakwana zaka 20. Izi zili choncho, nyumba yonse ya Isiraeli inayamba kulirira Yehova.+