1 Samueli 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo Sauli anauza Ahiya+ kuti: “Bweretsa likasa la Mulungu woona!”+ (Pakuti masiku amenewo likasa la Mulungu woona linali ndi ana a Isiraeli.)+
18 Pamenepo Sauli anauza Ahiya+ kuti: “Bweretsa likasa la Mulungu woona!”+ (Pakuti masiku amenewo likasa la Mulungu woona linali ndi ana a Isiraeli.)+