2 Samueli 3:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anthu onse anaona zimene zachitika, ndipo anaona kuti zimene mfumu ikuchita zili bwino. Mofanana ndi zonse zimene mfumuyo inachita, anthu onse anaona kuti izinso zili bwino.+
36 Anthu onse anaona zimene zachitika, ndipo anaona kuti zimene mfumu ikuchita zili bwino. Mofanana ndi zonse zimene mfumuyo inachita, anthu onse anaona kuti izinso zili bwino.+