1 Mafumu 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno mfumuyo inamuuza kuti: “Kodi ndikulumbiritse kangati kuti uzilankhula kwa ine zoona zokhazokha m’dzina la Yehova?”+
16 Ndiyeno mfumuyo inamuuza kuti: “Kodi ndikulumbiritse kangati kuti uzilankhula kwa ine zoona zokhazokha m’dzina la Yehova?”+