Salimo 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wasokoneza zolinga za anthu a mitundu ina.+Walepheretsa maganizo a mitundu ya anthu.+ 2 Atesalonika 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ichi n’chifukwa chake Mulungu walola kuti iwo anyengedwe ndipo azikhulupirira bodza,+