1 Mafumu 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Zedekiya mwana wa Kenaana anapanga nyanga zachitsulo n’kunena kuti: “Yehova wanena kuti,+ ‘Ndi nyanga izi mudzakankha Asiriya mpaka kuwatha.’”+
11 Ndiyeno Zedekiya mwana wa Kenaana anapanga nyanga zachitsulo n’kunena kuti: “Yehova wanena kuti,+ ‘Ndi nyanga izi mudzakankha Asiriya mpaka kuwatha.’”+