Yeremiya 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Pasuri anamenya mneneri Yeremiya+ ndi kumuika m’matangadza+ amene anali pa Chipata Chakumtunda cha Benjamini, cha m’nyumba ya Yehova. Maliko 14:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Pamenepo ena anayamba kumulavulira,+ kumuphimba nkhope ndi kumukhoma nkhonya. Iwo anali kunena kuti: “Losera!” Atamuwomba mbama, asilikali a pakhoti anamutenga.+ Machitidwe 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atamva zimenezi Hananiya mkulu wa ansembe, analamula anthu amene anaimirira pafupi naye kuti amubwanyule+ pakamwa.
2 Kenako Pasuri anamenya mneneri Yeremiya+ ndi kumuika m’matangadza+ amene anali pa Chipata Chakumtunda cha Benjamini, cha m’nyumba ya Yehova.
65 Pamenepo ena anayamba kumulavulira,+ kumuphimba nkhope ndi kumukhoma nkhonya. Iwo anali kunena kuti: “Losera!” Atamuwomba mbama, asilikali a pakhoti anamutenga.+
2 Atamva zimenezi Hananiya mkulu wa ansembe, analamula anthu amene anaimirira pafupi naye kuti amubwanyule+ pakamwa.