2 Mbiri 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Asa anamukwiyira wamasomphenyayo. Kenako anamuika m’ndende n’kumumanga m’matangadza+ popeza anamupsera mtima kwambiri chifukwa cha nkhani imeneyi.+ Pa nthawi yomweyo, Asa anayamba kuponderezanso+ anthu ake ena. Yeremiya 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Pasuri anamenya mneneri Yeremiya+ ndi kumuika m’matangadza+ amene anali pa Chipata Chakumtunda cha Benjamini, cha m’nyumba ya Yehova. Machitidwe 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ndi kugwira atumwiwo n’kuwatsekera m’ndende.+
10 Koma Asa anamukwiyira wamasomphenyayo. Kenako anamuika m’ndende n’kumumanga m’matangadza+ popeza anamupsera mtima kwambiri chifukwa cha nkhani imeneyi.+ Pa nthawi yomweyo, Asa anayamba kuponderezanso+ anthu ake ena.
2 Kenako Pasuri anamenya mneneri Yeremiya+ ndi kumuika m’matangadza+ amene anali pa Chipata Chakumtunda cha Benjamini, cha m’nyumba ya Yehova.