2 Mbiri 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komabe, pali zinthu zabwino+ zimene zapezeka mwa inu, chifukwa mwachotsa mizati yopatulika m’dzikoli,+ ndipo mwakonza mtima wanu kuti mufunefune Mulungu woona.”+
3 Komabe, pali zinthu zabwino+ zimene zapezeka mwa inu, chifukwa mwachotsa mizati yopatulika m’dzikoli,+ ndipo mwakonza mtima wanu kuti mufunefune Mulungu woona.”+