Oweruza 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “‘Choncho ndi Yehova Mulungu wa Aisiraeli amene anagonjetsa Aamori pamaso pa anthu ake Aisiraeli,+ ndipo iwe ukufuna kuwagonjetsa. Salimo 83:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anena kuti: “Bwerani tiwafafanize kuti asakhalenso mtundu,+Ndi kuti dzina la Isiraeli lisakumbukikenso.”+
23 “‘Choncho ndi Yehova Mulungu wa Aisiraeli amene anagonjetsa Aamori pamaso pa anthu ake Aisiraeli,+ ndipo iwe ukufuna kuwagonjetsa.
4 Iwo anena kuti: “Bwerani tiwafafanize kuti asakhalenso mtundu,+Ndi kuti dzina la Isiraeli lisakumbukikenso.”+