-
2 Mbiri 20:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Mawa mupite kukakumana nawo. Iwo akubwera ndipo adzera pampata wa Zizi. Mukawapeza kumapeto kwa chigwa chimene chili kutsogolo kwa chipululu cha Yerueli.
-