Yoswa 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Gulu la asilikali onyamula zida linali kuyenda patsogolo pa ansembe oimba malipenga, pamene gulu lina la asilikali linali kubwera pambuyo+ pa Likasa, kwinaku malipenga akuimbidwa mosalekeza.
9 Gulu la asilikali onyamula zida linali kuyenda patsogolo pa ansembe oimba malipenga, pamene gulu lina la asilikali linali kubwera pambuyo+ pa Likasa, kwinaku malipenga akuimbidwa mosalekeza.