Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako Ahaziya ali m’nyumba yake ku Samariya, anagwa+ kuchokera pachipinda chapadenga+ kudzera pachibowo chotchinga, ndipo anavulala. Atatero anatuma amithenga kuti: “Pitani kwa Baala-zebubu+ mulungu wa ku Ekironi,+ mukafunse+ ngati ndichire matenda angawa.”+

  • 2 Mafumu 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Atafika, Eliya anauza mfumuyo kuti: “Yehova wanena kuti: ‘Chifukwa chakuti watumiza anthu+ kukafunsa kwa Baala-zebubu mulungu wa ku Ekironi+ ngati kuti ku Isiraeli kulibe Mulungu amene ungafunsireko mawu ake, sutsika pabedi wakwerapo, chifukwa umwalira ndithu.’”

  • 2 Mbiri 19:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano Yehu+ mwana wa Haneni+ wamasomphenya,+ anapita kukaonekera kwa Mfumu Yehosafati ndipo anaifunsa kuti: “Kodi chithandizo chiyenera kuperekedwa+ kwa oipa, ndipo kodi muyenera kukonda anthu odana+ ndi Yehova?+ Chifukwa cha zimenezi Yehova wakukwiyirani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena