1 Mafumu 22:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Pomalizira pake, Yehosafati anagona ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide+ kholo lake. Kenako Yehoramu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
50 Pomalizira pake, Yehosafati anagona ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide+ kholo lake. Kenako Yehoramu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.