Genesis 43:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Abale akewo anakhala pansi pamaso pake, kuyambira woyamba kubadwa malinga ndi ukulu wake,+ mpaka wamng’ono malinga ndi msinkhu wake. Iwo anali kuyang’anana modabwa.
33 Abale akewo anakhala pansi pamaso pake, kuyambira woyamba kubadwa malinga ndi ukulu wake,+ mpaka wamng’ono malinga ndi msinkhu wake. Iwo anali kuyang’anana modabwa.