Genesis 27:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Udzakhalira moyo lupanga+ ndipo udzatumikira m’bale wako.+ Koma ukadzatopa ndi goli lake, udzalithyola ndi kulichotsa m’khosi mwako.”+
40 Udzakhalira moyo lupanga+ ndipo udzatumikira m’bale wako.+ Koma ukadzatopa ndi goli lake, udzalithyola ndi kulichotsa m’khosi mwako.”+