1 Mafumu 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kuchindikala kwa thankiyo kunali chikhatho* chimodzi.+ Mlomo wake unali ngati wa mphika wakukamwa ngati duwa.+ M’thankiyo munkalowa+ madzi okwana mitsuko* 2,000.+
26 Kuchindikala kwa thankiyo kunali chikhatho* chimodzi.+ Mlomo wake unali ngati wa mphika wakukamwa ngati duwa.+ M’thankiyo munkalowa+ madzi okwana mitsuko* 2,000.+