2 Mbiri 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Amaziya+ anafunsa munthu wa Mulungu woonayo kuti: “Nanga bwanji za matalente 100 amene ndapereka kwa asilikali a ku Isiraeli aja?”+ Munthu wa Mulungu woonayo anayankha kuti: “Yehova akhoza kukupatsani zambiri kuposa pamenepa.”+
9 Pamenepo Amaziya+ anafunsa munthu wa Mulungu woonayo kuti: “Nanga bwanji za matalente 100 amene ndapereka kwa asilikali a ku Isiraeli aja?”+ Munthu wa Mulungu woonayo anayankha kuti: “Yehova akhoza kukupatsani zambiri kuposa pamenepa.”+