1 Mafumu 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’nthawi ya mafumu a Yuda. 2 Mafumu 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nkhani zina zokhudza Yehoasi ndi zonse zimene anachita zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda.
29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’nthawi ya mafumu a Yuda.
19 Nkhani zina zokhudza Yehoasi ndi zonse zimene anachita zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda.