1 Mafumu 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Davide anagona limodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide.+ 1 Mafumu 11:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kenako Solomo anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide+ bambo ake. Kenako mwana wake Rehobowamu,+ anayamba kulamulira m’malo mwake.
43 Kenako Solomo anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide+ bambo ake. Kenako mwana wake Rehobowamu,+ anayamba kulamulira m’malo mwake.