Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “Mukadzafufuza Yehova Mulungu wanu muli kumeneko, mudzam’pezadi,+ chifukwa mudzam’funafuna ndi mtima wanu wonse ndiponso moyo wanu wonse.+

  • 2 Mbiri 14:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho iye anauza Ayuda kuti: “Tiyeni timange mizindayi ndi mipanda+ yoizungulira. Timangenso nsanja+ ndipo tipange makomo a zitseko ziwiriziwiri ndi mipiringidzo.+ Malo m’dzikoli akadalipo chifukwa tafunafuna Yehova Mulungu wathu.+ Tam’funafuna ndipo watipatsa mpumulo pakati pa adani athu onse otizungulira.”+ Chotero iwo anamangadi ndipo zinthu zinawayendera bwino.+

  • 2 Mbiri 17:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iye anafunafuna Mulungu wa bambo ake+ ndipo anayenda+ motsatira chilamulo chake, sanatsatire zochita za Aisiraeli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena