Numeri 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uwerenge kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo,+ aliyense woyenerera kupita kunkhondo pakati pa Aisiraeli.+ Iweyo ndi Aroni muwalembe m’kaundula malinga ndi magulu awo a asilikali. 2 Samueli 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano Yowabu anapereka chiwerengero chonse+ cha anthu kwa mfumu. Aisiraeli analipo 800,000, amuna amphamvu ogwira lupanga, ndipo amuna a Yuda analipo 500,000.+
3 Uwerenge kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo,+ aliyense woyenerera kupita kunkhondo pakati pa Aisiraeli.+ Iweyo ndi Aroni muwalembe m’kaundula malinga ndi magulu awo a asilikali.
9 Tsopano Yowabu anapereka chiwerengero chonse+ cha anthu kwa mfumu. Aisiraeli analipo 800,000, amuna amphamvu ogwira lupanga, ndipo amuna a Yuda analipo 500,000.+