28 Panalinso zinthu zonse zimene Samueli wamasomphenya,+ Sauli mwana wa Kisi, Abineri+ mwana wa Nera, ndi Yowabu+ mwana wa Zeruya+ anaziyeretsa kukhala zopatulika. Chilichonse chimene munthu anachiyeretsa chinali kuyang’aniridwa ndi Selomiti ndi abale ake.