Levitiko 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Munthu akatuluka zotupa, kapena nkhanambo,+ kapena chikanga pakhungu lake, ndipo chasintha n’kukhala nthenda ya khate,+ azibwera naye kwa Aroni wansembe, kapena kwa mmodzi wa ana ake amenenso ndi ansembe.+
2 “Munthu akatuluka zotupa, kapena nkhanambo,+ kapena chikanga pakhungu lake, ndipo chasintha n’kukhala nthenda ya khate,+ azibwera naye kwa Aroni wansembe, kapena kwa mmodzi wa ana ake amenenso ndi ansembe.+