Levitiko 14:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Mukakafika m’dziko la Kanani,+ limene ine ndikukupatsani kuti likhale lanu,+ ndipo ndikakaika nthenda ya khate m’nyumba iliyonse m’dziko lanulo,+ Deuteronomo 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova adzakulanga ndi chifuwa chachikulu,+ kuphwanya kwa thupi koopsa, kutupa, kutentha thupi kwambiri, lupanga,+ mphepo yotentha yowononga mbewu+ ndi matenda a mbewu.+ Zimenezi zidzakusautsa kufikira utawonongeka. Deuteronomo 28:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Yehova adzakulanga ndi zithupsa zonyeka m’mawondo onse ndi m’ntchafu monse. Matenda amenewa adzayambira kumapazi mpaka paliwombo, ndipo sudzachira.+
34 “Mukakafika m’dziko la Kanani,+ limene ine ndikukupatsani kuti likhale lanu,+ ndipo ndikakaika nthenda ya khate m’nyumba iliyonse m’dziko lanulo,+
22 Yehova adzakulanga ndi chifuwa chachikulu,+ kuphwanya kwa thupi koopsa, kutupa, kutentha thupi kwambiri, lupanga,+ mphepo yotentha yowononga mbewu+ ndi matenda a mbewu.+ Zimenezi zidzakusautsa kufikira utawonongeka.
35 “Yehova adzakulanga ndi zithupsa zonyeka m’mawondo onse ndi m’ntchafu monse. Matenda amenewa adzayambira kumapazi mpaka paliwombo, ndipo sudzachira.+