2 Mafumu 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehoasi anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova, masiku onse amene wansembe Yehoyada anali kumulangiza.+ 2 Mbiri 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova anapitiriza kukhala ndi Yehosafati+ chifukwa anayenda m’njira zimene Davide kholo lake+ anayenda kalekale, ndipo sanafunefune Abaala.+
2 Yehoasi anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova, masiku onse amene wansembe Yehoyada anali kumulangiza.+
3 Yehova anapitiriza kukhala ndi Yehosafati+ chifukwa anayenda m’njira zimene Davide kholo lake+ anayenda kalekale, ndipo sanafunefune Abaala.+