2 Mafumu 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Koma sanachotse malo okwezeka.+ Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo. Iye ndiye anamanga chipata chakumtunda cha nyumba ya Yehova.+
35 Koma sanachotse malo okwezeka.+ Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo. Iye ndiye anamanga chipata chakumtunda cha nyumba ya Yehova.+