Deuteronomo 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 dziko la tirigu, balere, mphesa, nkhuyu ndi makangaza,*+ dziko la maolivi opangira mafuta ndiponso la uchi,+ 2 Mbiri 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo tirigu, balere, mafuta, ndi vinyo, zimene inu mbuye wanga mwalonjeza, zitumizeni kwa ife akapolo anu.+
8 dziko la tirigu, balere, mphesa, nkhuyu ndi makangaza,*+ dziko la maolivi opangira mafuta ndiponso la uchi,+
15 Ndipo tirigu, balere, mafuta, ndi vinyo, zimene inu mbuye wanga mwalonjeza, zitumizeni kwa ife akapolo anu.+