2 Mafumu 15:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pomalizira pake, Yotamu anagona pamodzi ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide kholo lake. Kenako Ahazi+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
38 Pomalizira pake, Yotamu anagona pamodzi ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide kholo lake. Kenako Ahazi+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.