Yesaya 58:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Kusala kudya kumene ine ndimafuna n’kotere: Mumasule maunyolo ozunzira anzanu,+ mumasule zingwe za goli,+ mumasule anthu opsinjika kuti azipita kwawo,+ ndipo goli lililonse mulithyole pakati.+ Yeremiya 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma inu munatembenuka ndi kuchita zolungama pamaso panga mwa kulengeza ufulu, aliyense kwa mnzake. Munachita pangano pamaso panga,+ m’nyumba imene ikutchedwa ndi dzina langa.+
6 “Kusala kudya kumene ine ndimafuna n’kotere: Mumasule maunyolo ozunzira anzanu,+ mumasule zingwe za goli,+ mumasule anthu opsinjika kuti azipita kwawo,+ ndipo goli lililonse mulithyole pakati.+
15 Koma inu munatembenuka ndi kuchita zolungama pamaso panga mwa kulengeza ufulu, aliyense kwa mnzake. Munachita pangano pamaso panga,+ m’nyumba imene ikutchedwa ndi dzina langa.+