Yesaya 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Manase adzadya Efuraimu ndipo Efuraimu adzadya Manase. Awiriwa adzaukira Yuda pamodzi.+ Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere, ndipo dzanja lake lidakali lotambasula.+
21 Manase adzadya Efuraimu ndipo Efuraimu adzadya Manase. Awiriwa adzaukira Yuda pamodzi.+ Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere, ndipo dzanja lake lidakali lotambasula.+