Ekisodo 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo mkwiyo wanga udzakuyakirani,+ ndipo ndidzakuphani ndithu ndi lupanga, kuti akazi anu akhale akazi amasiye ndiponso ana anu akhale ana amasiye.+ Yoswa 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi inuyo tsopano mukufuna kubwerera n’kusiya kutsatira Yehova? Mukapandukira Yehova lero, ndiye kuti mawa adzakwiyira khamu lonse la Isiraeli.+ Aroma 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+
24 Pamenepo mkwiyo wanga udzakuyakirani,+ ndipo ndidzakuphani ndithu ndi lupanga, kuti akazi anu akhale akazi amasiye ndiponso ana anu akhale ana amasiye.+
18 Kodi inuyo tsopano mukufuna kubwerera n’kusiya kutsatira Yehova? Mukapandukira Yehova lero, ndiye kuti mawa adzakwiyira khamu lonse la Isiraeli.+
5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+