Yesaya 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova adzabweretsera iweyo,+ anthu ako, ndi nyumba ya bambo ako masiku amene sanakhaleponso kuyambira tsiku limene Efuraimu anapatukana ndi Yuda.+ Iye adzakubweretserani mfumu ya Asuri.+
17 Yehova adzabweretsera iweyo,+ anthu ako, ndi nyumba ya bambo ako masiku amene sanakhaleponso kuyambira tsiku limene Efuraimu anapatukana ndi Yuda.+ Iye adzakubweretserani mfumu ya Asuri.+