2 Mafumu 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamenepo Hezekiya mfumu ya Yuda anachotsa zitseko za kachisi wa Yehova+ ndi mafelemu ake, zimene iye anazikuta+ ndi golide, n’kupereka golideyo kwa mfumu ya Asuri.
16 Pamenepo Hezekiya mfumu ya Yuda anachotsa zitseko za kachisi wa Yehova+ ndi mafelemu ake, zimene iye anazikuta+ ndi golide, n’kupereka golideyo kwa mfumu ya Asuri.