2 Mbiri 31:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Hezekiya anachita zimenezi mu Yuda yense, ndipo anapitiriza kuchita zabwino,+ zoyenera+ ndi zokhulupirika+ pamaso pa Yehova Mulungu wake. Miyambo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Woyenda ndi mtima wosagawanika adzayenda popanda chomuopseza,+ koma wokhotetsa njira zake adzadziwika.+
20 Hezekiya anachita zimenezi mu Yuda yense, ndipo anapitiriza kuchita zabwino,+ zoyenera+ ndi zokhulupirika+ pamaso pa Yehova Mulungu wake.
9 Woyenda ndi mtima wosagawanika adzayenda popanda chomuopseza,+ koma wokhotetsa njira zake adzadziwika.+