34 Zitseko ziwirizo zinali za matabwa a mitengo yofanana ndi mkungudza.+ Zitseko ziwiri za khomo limodzi zinkayenda pamiyendo yake, ndipo zitseko ziwiri za khomo linalo zinkayendanso pamiyendo yake.+
24 Kuwonjezera apo, Ahazi anasonkhanitsa ziwiya+ za m’nyumba ya Mulungu woona+ n’kuziphwanyaphwanya. Komanso anatseka zitseko+ za nyumba ya Yehova. Kenako anakadzimangira maguwa ansembe m’makona onse a mu Yerusalemu.+