Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+ 2 Mbiri 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 M’kupita kwa nthawi iwo anasiya nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo awo n’kuyamba kutumikira mizati yopatulika+ ndiponso mafano.+ Chotero mkwiyo wa Mulungu unagwera Yuda ndi Yerusalemu chifukwa cha kupalamula kwawoko.+
15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+
18 M’kupita kwa nthawi iwo anasiya nyumba ya Yehova Mulungu wa makolo awo n’kuyamba kutumikira mizati yopatulika+ ndiponso mafano.+ Chotero mkwiyo wa Mulungu unagwera Yuda ndi Yerusalemu chifukwa cha kupalamula kwawoko.+