Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Itanitsa fuko la Levi+ ndipo uwapereke kwa wansembe Aroni kuti azimutumikira.+

  • Numeri 18:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Utengenso abale ako a fuko la Levi, amtundu wa bambo ako, kuti azikhala pafupi ndi inu. Azitumikira+ iweyo limodzi ndi ana ako pachihema cha Umboni.+

  • Numeri 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Inetu ndatenga abale anu Alevi, mwa ana a Isiraeli,+ ndipo ndawapereka kwa inu monga mphatso yanu.+ Iwowa akhala operekedwa kwa Yehova kuti atumikire pachihema chokumanako.+

  • Deuteronomo 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Pa nthawi imeneyo, Yehova anapatula fuko la Levi+ kuti lizinyamula likasa la pangano la Yehova,+ liziima pamaso pa Yehova pom’tumikira,+ ndi kuti lizidalitsa m’dzina lake kufikira lero.+

  • Luka 12:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Koma amene sanadziwe+ ndipo wachita zinthu zofunika kum’kwapula zikoti, adzam’kwapula zikoti zochepa.+ Inde, aliyense amene anapatsidwa zambiri, zambirinso zidzafunika kwa iye.+ Ndipo aliyense amene anthu anamuika kuyang’anira zinthu zochuluka, anthuwo adzafunanso zochuluka kwa iye.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena