1 Mbiri 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero Alevi anatenga Hemani+ mwana wa Yoweli n’kumuika pamalo ake. Kenako, pa abale ake, anatengapo Asafu+ mwana wa Berekiya n’kumuika pamalo ake. Pa abale awo, ana a Merari, anatengapo Etani+ mwana wa Kusaya n’kumuika pamalo ake. 1 Mbiri 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa ana a Asafu, anatengapo Zakuri, Yosefe,+ Netaniya, ndi Asarela.+ Ana ake amenewa anali kuyang’aniridwa ndi Asafuyo,+ amenenso anali mneneri wa mfumu.
17 Chotero Alevi anatenga Hemani+ mwana wa Yoweli n’kumuika pamalo ake. Kenako, pa abale ake, anatengapo Asafu+ mwana wa Berekiya n’kumuika pamalo ake. Pa abale awo, ana a Merari, anatengapo Etani+ mwana wa Kusaya n’kumuika pamalo ake.
2 Pa ana a Asafu, anatengapo Zakuri, Yosefe,+ Netaniya, ndi Asarela.+ Ana ake amenewa anali kuyang’aniridwa ndi Asafuyo,+ amenenso anali mneneri wa mfumu.